Okla

Okla Everything

Benoni Samara Samara muma shop awunzeni ma bwana lero lonkha mupumeko
06/06/2026

Benoni Samara Samara muma shop awunzeni ma bwana lero lonkha mupumeko

god is good
06/06/2026

god is good

spanner Malawi. mnthutu uyu ineyo ndatitu ineyo sindikuonapo cholakwika China chilichose APA . amalawi tiyeni tingokhara...
03/06/2026

spanner Malawi. mnthutu uyu ineyo ndatitu ineyo sindikuonapo cholakwika China chilichose APA . amalawi tiyeni tingokhara ndi kanzimu Kena kake tisatengere Kuti uja ndiwontchuka ndeno Ngati alemba pasamba Lake basi kumangolondola zilinzotse ayi. uyutu alibe manege that is big problem Ngati nokha mungalione vutoli Koma zimene akumapanga spannezi akanakhara Emmi Debo or Rita Tamia miracle chinga . panotu bwez mukumaona ma ikk ndima hipapu ndi mabungwe womwe kulowerera chithandinzo basi kufuna nyemba basi . inu amalawi kutitu muonesese nokha ndatitu nokha . uyutu akachoka koyendako kamene akapedzako ndikuona muma social media akuthandizako wonsawuka akumapangatu izi spanner. Koma ndiliti munavapo nzoti Rita Tamia miracle chinga aperekapo chopereka kwaosauka .. amalawi kuthandinza poyamba paja sikuti tinasiyirapopo ayi or kuthandinza sikuti ndi ndalama zokha ayi Koma kumupasa zeru kumene kumufunila zabwino ndithandinzo larikulu ndi2 πŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™πŸ™πŸ™πŸ™πŸ™

03/06/2026

akazi ife siolakwa wolakwa ndi amunawa potitenga kwa2 kutiyika pankhomo lakwawo

02/06/2026

khuda myawa ndi Tamia amatiyenda zapasi

🚨🀯 Man United and Vinicius Junior 😳Reports claim intermediaries have made contact with Manchester United over a potentia...
01/06/2026

🚨🀯 Man United and Vinicius Junior 😳

Reports claim intermediaries have made contact with Manchester United over a potential deal for Real Madrid forward Vinicius Jr this summer.

ndipo awakana Ku Limpopo akutitu Ngati...
01/06/2026

ndipo awakana Ku Limpopo akutitu Ngati...

kamupane yija Kuno alowa akuba ndikuba Koma CcTV palibe yaonesako
01/06/2026

kamupane yija Kuno alowa akuba ndikuba Koma CcTV palibe yaonesako

Address

Mzimba
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Okla posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share