Atie Budget Style Mw

Atie Budget Style Mw We specialize in High quality new and second- hand dresses and clothing for women who love to look fabulous.

Based in Area 49 , Lilongwe we sell and deliver anywhere in Malawi.

Available in Lilongwe Area 49 you can call or text on 0997571383 or 0882471485
15/05/2026

Available in Lilongwe Area 49 you can call or text on 0997571383 or 0882471485

WhatsApp 0997571383
12/05/2026

WhatsApp 0997571383

Anena kuti kuvala zovala zatsopano pa khilisimisi zinatha, mumufotokozere kuti Manama ndipo mudzidzimutseni ndi tima dre...
19/12/2025

Anena kuti kuvala zovala zatsopano pa khilisimisi zinatha, mumufotokozere kuti Manama ndipo mudzidzimutseni ndi tima dress yabwino tosabowola nthumba iti

Pa ma plan Anu a Weekend, Dress lilipo kale loti muvale kapena muvala dzomwe dzija.Anzanu awa kukondwa ndi katundu wathu...
12/12/2025

Pa ma plan Anu a Weekend, Dress lilipo kale loti muvale kapena muvala dzomwe dzija.
Anzanu awa kukondwa ndi katundu wathu.

Tilipotu towoneka bwino, kutchena ndi wekha. Contact us or visit us in Area 49.
08/12/2025

Tilipotu towoneka bwino, kutchena ndi wekha. Contact us or visit us in Area 49.

New arrivals🔥🔥located in Lilongwe area 49 Dubai
18/11/2025

New arrivals🔥🔥located in Lilongwe area 49 Dubai

Kusafusilidwa kwinakutu ndikavalidwetu😂😂.Week yangoyamba iyi tasankhani yanu kenakomutiyimbire phone,  ticheze.
27/10/2025

Kusafusilidwa kwinakutu ndikavalidwetu😂😂.
Week yangoyamba iyi tasankhani yanu kenakomutiyimbire phone, ticheze.

Kuvala bwinotu sikuchita kufuna mukhale ndi zochuluka. Tatengani ma dress awa mutchene weekend imeneyi pa mtengo omveler...
24/10/2025

Kuvala bwinotu sikuchita kufuna mukhale ndi zochuluka. Tatengani ma dress awa mutchene weekend imeneyi pa mtengo omvelera. Kulikonseko tiuzeni tibweretsa.

 Chikondi cha Mayi ndichakuya.
15/10/2025


Chikondi cha Mayi ndichakuya.

Kodi nthawi yovala dza blue yatha kale, kapena kuli zina zochitika zofunika ma dress A BLUE. Tabwerani mudzapeze anu abw...
07/10/2025

Kodi nthawi yovala dza blue yatha kale, kapena kuli zina zochitika zofunika ma dress A BLUE. Tabwerani mudzapeze anu abwino pa mtengo womvelera?

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Atie Budget Style Mw posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category