08/10/2025
POEM
🧕 MTSUNGWANA OSAVALA HIJJAB🧕
ukamuona mtsungwana osavala hijjab
ameneo akukokedwa ndi jabu jabu
mpangeni k*t adziwe malemba amchitabu
atavala sindiketi ngati kapu
ine ndilibe naye mau
mtsungwana osavala hijjab
may we goo!!!!