Itz halima beib

Itz halima beib Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Itz halima beib, Women's clothes shop, Vincentnyirenda17gmail. com, Mzuzu.

Tangoika opanda chifukwa 🤔
06/04/2024

Tangoika opanda chifukwa 🤔

TUNO akuti...;1). Oimba aakazi akumagonana ndi ma Producer cholinga awapange record nyimbo zawo ulere.2). Ine winawake k...
13/03/2024

TUNO akuti...;

1). Oimba aakazi akumagonana ndi ma Producer cholinga awapange record nyimbo zawo ulere.

2). Ine winawake kwawo kuli wayilesi, anandinyengerera kuti nkatsope ujeni kuti azindisewerera nyimbo zanga, ndipo adakhaulatu! Namukanira m'maso muli mbeee

3). Charisma tidagonako chipinda chimodzi usiku onse, ndipo ndidasintha zovala iyeyo ali mchipinda mommo, koma sitinasosolane ayi! Ameneuja ali ngati mchimwene wanga.

4). Ineyo! Rango uja! kungokumanizana naye, nzamuthyapa makofi, amandinyasa kwambiri ameneuja! Amazimva!

5). Ngati a Teddy amazinamiza kuti ndi a Ex anga amangozivuta! Ine ma Ex anga ndi awiri okha ndipo a Teddy wo anali ngati Rebound chabe, tinawalawitsa poti ankanyengerera, ankavesa chisoni.

6). Uyu amazitcha kuti “Chiphadzuwa cha Malawe” anapita ku Nigeria, kumanamizira kuti akapanga represent Malawi pa za maimbidwe chonsecho amakagulitsa nyemba kwa azibambo Mxiew!!! Ndi Hule ameneuja!

7). Amuna amene adalowako mwa ineyo sakukwana nkomwe olo khumi ‘10’ ayi, ndi asanu ndi atatu ‘8’ okha.

koma ziliko😂😂

Address

Vincentnyirenda17gmail. Com
Mzuzu

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Itz halima beib posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share