Dor's Catalogue

Dor's Catalogue We stock packaging papers, herbs and Spices for your health and flavor. We are in Limbe Phalombe hardware room 14. Call/Whatsapp: +265 993555560

Kulitu somph sweets Kuno akasi
14/05/2026

Kulitu somph sweets Kuno akasi

Watch, follow, and discover more trending content.

13/05/2026

Timaphunzitsa kaphikidwe ka sweet Malambe Snacks lamululungu lililonse. Tiyeni tikhale limodzi lamululungu likubwerali Insha'Allah
Pa phone(online): mk20, 000
Pamaso (physical): mk45, 000
Chonde uzani anzanu

10/05/2026

Yes Akasi
Tende alipo. Pezani wanu kuchokera Ku Dor's Herbs and Spices

08/05/2026

Zifukwa Zina zomwe elastic wa Malo obisika a munthu wankazi amakhwepera:
1. Matenda
2. Kubeleka
3. Kukula (Age)


Mk6, 500

19/04/2026

Ife ngati anthu tiyeni tipange mbali yathu kwinaku tikumupempha Namalenga, poti iye ali ndi kuthekela kopanga zinthu
WITHOUT THE MEANS
WITH THE MEANS and
THROUGH THE MEANS

Female fertility booster (100g): mk25, 000
Dor's Catalogue Doreen Imaan

15/04/2026

Mwenje Salt
200g: Mk20, 000
Tili mu Limbe mmwamba mwa Phalombe Hardware room 15. Kutali timatumiza.

09/04/2026

Kuonjezera magazi
Kupweteka Kwa msana
Nyamakazi
Maso
Kukulitsa tsitsi
Kusalalits akhungu
Kunfotchulapo zochepa chabe...

28/03/2026

Yafika nthawi ya Maungu.
Tili mu Limbe mmwamba mwa Phalombe Hardware room 15. Kutali timatumiza

27/02/2026

Dzaguleni Henna wabwino, owala komanso okhalitsa.

Address

Blantyre
Blantyre

Opening Hours

Monday 08:00 - 17:00
Tuesday 08:00 - 17:00
Wednesday 08:00 - 17:00
Thursday 08:00 - 17:00
Friday 08:00 - 17:00
Saturday 09:00 - 17:00
Sunday 10:00 - 17:00

Telephone

+265993555560

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Dor's Catalogue posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Dor's Catalogue:

Share