21/04/2026
Pamene Mbalame ilimoyo, imadya Nyerere.
Pamene Mbalame yafa, Nyerere zimaidya
Nthawi ndi Zochitikachitika zimatha kusintha munthawi iliyose. Osamachepetsa kapena kupweteka ena mmoyo. M***a kukhala amphavu lero, Koma osaiwala kuti Nthawi nde yamphavu kwambiri
Zikomo.🙏🙏❤️❤️
MR EYAH Creatives