Cwagniser

Cwagniser Story and photo concepts

18/04/2023

Zimangoona kuvuta koma zimafunika wife material asamakhale ndi ma likes oposa 100 pa picture yake.

18/04/2023

Ngati wakupatsa Nambala ndiye Kuti walola ameneyo, chifukwa kulibe Company Yomwe imapereka work suit ngati ntchito Palibe.

18/04/2023

Ambiri pano bwenzi muli ndi ana koma tikudziwa zomwe munapanga ๐Ÿ˜‚

16/04/2023

Never ask a girl whether she has a boyfriend. Just join the queue the winner will be announced in Church ๐Ÿ˜Š

KWACHA!!

15/04/2023

Post yanga kuzangopanga comment sing'anga ndizapha ๐Ÿ™„๐Ÿ™„๐Ÿ™„

14/04/2023

Ndalama or usamwele mowa imathabe๐Ÿ’€

14/04/2023

Name One Artist From India
๐Ÿ˜ญ
๐Ÿ‘•
๐Ÿ‘–

13/04/2023

Osamapepesa
Pazinthu zoti
Mukhoza kusova
Ndi mbama๐Ÿ˜‚

12/04/2023

Ndimamuuza mzimayi wa restaurant monong'ona koma iye wangofikira kushauta "nsima ya fafandede palibe!!!!" Ine aaaaaah๐Ÿ™„๐Ÿ˜ฒ

Kukhala amatelo ๐Ÿ˜๐Ÿ˜Ž๐Ÿ‘ฎ๐Ÿ„

12/04/2023

Ndimasaka network m'munda mwa Aneba nde mwangozi potuluka ndapezeka ndi Chimanga 10 ndi maungu awiri๐Ÿ˜ข

Address

Area 25
Lilongwe

Telephone

+265991395438

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Cwagniser posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share