Ndinenenji

Ndinenenji TIUWUNI KILANE ZACHIPULUMUTSO CHATHU.

18/01/2022

Nthawi yakwana liyambeno kugwila ntchito group yi

Chonde abale esetsani kusakasaka ufumu wa Mulengi funitsitsani kudziwa kuti wadza ndindani m'ntendele. Amen
11/02/2020

Chonde abale esetsani kusakasaka ufumu wa Mulengi funitsitsani kudziwa kuti wadza ndindani m'ntendele. Amen

08/01/2020

Mulungu adzalanga mwana chifukwa cha atateake masiku ano athusakudziwa Mulungu wawo, kodi Inu Mulungu wanu ndindani?

05/01/2020

Moninose abale mwambuye
ngati mulibwino ndili okondwa.

ndafuna tigawane mawu ogulila moyo vuto lathu ndikunyozela ndiposo sitidziwa kuti ndizoona koma timadzitsutsa zoona ndiku tsata zosadziwa kutsogolo
kwe,

TAVANI KANKHANI AKA

Panali nkhalamba ina yakale
agogowa anakhala pa mpando, panyumba yawo anaona nkhuku komaso chiwala pabwalo lanyumbayo posa khalitsa anoona nkhuku yinja ikuthamangitsa chiwala chija
mosalekeza chiwala chikati chidumphe nkhuku ilipambuyo
zita zunglitsana kwakanthawi
chiwala chinatopa mwamwayi
chinadumpha ndiku gwela mubotolo lagilasi nkhuku yija inayesele kupisa mulomo koma
mutuwake sunakwanitsa kulowa kom itayesa ndikutopa ,

TIYENIBE
inapuma pasipa mntengo chiwalaso chitazindikila kuti chili
chotetezeka nachoso chinapuma koma kamba kakudziva kuti chapeza mphavu

chinadumpha ndikutuluka nayoso nkhuku itaona inanyamuka ndikuyambaso kuthamangitsa chiwalacho koma poti kunalibe maloena oti chiwalacho chingapulumuke
nkhuku yija inagwila chiwalacho ndiku chipha ndikuchidya.

TANTHAUZO LANTHANOYI

Agogo aja akuyimila mulengi amene amayang'anila chilengedwe chose nkhuku yija ikuyimila satana amene amatilondalonda palipase kufunakuti tisiye malamulo amulengi kuti titsate zachikunja
kuti tionongeke botolo lagilasi lija likuimila malamulo amulengi
poti ngati ulimnkati mwamalamulo amulengi umakhala otetezeka pot umakhala opulumuka kumisa mpa yadziko kudziva mphavu kuja kuyimila munthu amene amadziva kupelewela mntendele mumalamulo amulengi ndiku yambaso kutsata njila zadziko kumapeto ake umadyedwa ndi chilango ndikutsikila kumanda.

ODALA NDIWO AVETSA MAWU
WA .Ame
Palibe ofunika popanda make
zamdziko ndi zachabe chabe
tikonde malamulo amulengi.
TIDZAKHALA NDI MOYO .
Ine ganizani B N zenengeya m,balewanu mwambuye nditi mntendele ndiokoma.

26/12/2019

Kuzindikila chilungamo kumapatsa zelu fusani muzayankhidwa ngakhale loto mudzamasulilidwa musasawutsike ndi kusinkhasinkha.Amen

19/12/2019

Kodi panyama zose nyama yazelu ndinyama yanji? nanga ndi chifukwa chani ili yazelu kuposa nyama zina?

06/12/2019

Tifufuze zokhudza chiyambi chadziko komaso mathelo ake ndichiyambi chadziko lantendele ndikudziwa maweluzo ake tipatsane mafuso ndi kuyankhana mwamzelu.amen

Chilungamo chikambidwe Malawi azindikile choonadi.
05/12/2019

Chilungamo chikambidwe Malawi azindikile choonadi.

Address

M 1
Lilongwe

Telephone

+265992356905

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ndinenenji posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share