Mr Designer tailoring shop

Mr Designer tailoring shop Timasoka zovala zakumtima kwanu china chilichonse mungafune timapanga by Mr Designer

16/04/2022

wawawa pipo

26/03/2022

halla me on.wap

26/03/2022

mr designer on fire kupanga zigin

09/03/2022

Azanu akubwera kuzaphuzira musasalire tipezen malo adakalipo kuno mr designer

28/02/2022

Tiyeni achinyamata tisafe manja kuphuzira pantengo wa ziiiiiiiii tikakhuren basi

28/02/2022

Tsiku lija kafika ndi mawa maclass akuyamba tikamati 8:00am tikhara kuti tayamba kuphuzitsa kusoka

16/02/2022

Tikhara tikuphuzitsa kusoka mwezi wamawau murch pamtengo wa bho tikupezekera mu M1 load Panayele kuti muziwe zambiri m***a kutilakhura pa 0994284887 osafa manja achinyamata

05/02/2022

Chilundu wear for sale Cha anyamata & azimayi zilipo🤸🤸

24/01/2022

Tinchena pano Basi 2022 on fire

24/01/2022
04/12/2021

tikhara tikusoka zovara zogulitsa kuyambira pa 20.mwezi uno wazisangalaro monga ma dress,siket,trousers,shirt and more

22/09/2021

Thanks all guyz

Address

M1 Road
Lilongwe

Telephone

+265994284887

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mr Designer tailoring shop posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share