Van Victor

Van Victor Gospel Musician πŸŽΆπŸ“ŒπŸ–‡οΈπŸ”₯

Any Business +265884083263

Based In Ntcheu πŸ€™
(1)

Fans Yanga isamachite kusowa bundle ine ndilipo Mayazi ' pitilizani kuponya ma number anu TNM komaso Airtel πŸ“±πŸ˜Ž Aguru
18/05/2026

Fans Yanga isamachite kusowa bundle ine ndilipo
Mayazi ' pitilizani kuponya ma number anu TNM komaso Airtel πŸ“±

😎 Aguru

18/05/2026

Osadandaula ma number anuwa ndikuwalembatu ✍️

18/05/2026

Ndakonzeka lero kugawa bundle πŸ“± mkale nazisowa izii ' osayiwala kupanga likes chimene tatumiza Kuti ma points anu adzichuluka 🀝

Full time NYASA BULLETS 0:0 RED LIONS βš½πŸ“Œ
17/05/2026

Full time

NYASA BULLETS 0:0 RED LIONS

βš½πŸ“Œ

Ayi Arsenal singafike ma final a champion πŸ† Lero anthu ali buys kugura ma tickets πŸŽ«πŸ˜€πŸ™Ayi Arsenal premier League sidzaten...
17/05/2026

Ayi Arsenal singafike ma final a champion πŸ†
Lero anthu ali buys kugura ma tickets πŸŽ«πŸ˜€πŸ™

Ayi Arsenal premier League sidzatengaso πŸ†
pano ili 79 points only 2 games Kuti itenge πŸ˜€πŸ™

pano atipangira create iziiii πŸ‘‡akuti tiwope πŸ˜‚

And one day I will be a world-class artistAnd I believe many will call me to sing for you 😎🀚Ndipo tsiku lina ndidzakhala...
17/05/2026

And one day I will be a world-class artist
And I believe many will call me to sing for you 😎🀚

Ndipo tsiku lina ndidzakhala artist wa dziko lonse
Ndipo ndikukhulupilira ' ambili mudzanditana dzakuyimbileni 🀝

Aguru, Aguru mwadzuka bwanji lero 🀝?ine ndadzuka bwino ndithudi πŸ–οΈKaya inu mulikuti anzanthu lero ' makamaka mulipa line...
17/05/2026

Aguru, Aguru mwadzuka bwanji lero 🀝?
ine ndadzuka bwino ndithudi πŸ–οΈ

Kaya inu mulikuti anzanthu lero ' makamaka muli
pa line?

😎 Aguru

16/05/2026

Chelsea sapanganika😭

16/05/2026

Osayiwala kupanga likes chimene tatumiza 🀝

Dear Chelsea Football Club , we Arsenal fans are behind you today 😎Anita Phoenix Mabedi ⚽Menyani ana lero 😁 ndadzuka osa...
16/05/2026

Dear Chelsea Football Club , we Arsenal fans are behind you today 😎

Anita Phoenix Mabedi ⚽

Menyani ana lero 😁 ndadzuka osangalala relo uyu
Ali pa line uyu 🫡 ndikugayileko 10 pin πŸ“Œ bundle

Address

Lilongwe

Telephone

+265888121268

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Van Victor posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Van Victor:

Share