Faluku

Faluku Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Faluku, Midrand.

Rapper who died of drag ods
27/01/2026

Rapper who died of drag ods

Pamene Boma la China layamba kufufuza Mkulu wao wa Asilikali pa Mlandu ogulitsa information ya Military Ku USA , mphekes...
26/01/2026

Pamene Boma la China layamba kufufuza Mkulu wao wa Asilikali pa Mlandu ogulitsa information ya Military Ku USA , mphekesela zayamba kumveka kuti Asilikaliwa alipo angapo amene akuganizilidwa kuti afuna kulanda Boma ndi kugwetsa president

16/01/2026

“Nkhani Ya Bambo Waku Mchinji Ine Lawyer Sylvester Ayuba Ndimuyimira Ulere Ndiosalakwa”

-Khoti la a Magistrate ku Mchinji lapeza Ernest Chimpeni wazaka 37 ndi mlandu wogwirira mwana atasimikiza kuti mtsikanayo anali wosakwana zaka 18, ngakhale iye atanena kuti ali ndi zaka 19 komanso kuwonetsa chiphaso cha mzika cha dziko chomwe chimanena kuti anabadwa mu 2006.

Khoti linamva kuti Chimpeni anayamba zokonzekera ukwati ndi banja la mtsikanayo ndipo anapereka K30,000 ndi nkhuku ngati gawo la mwambo wa malowolo, koma pambuyo pake anazindikira kuti mtsikanayo anali ndi pakati pa mwamuna wina kenaka anapita kwawo kwa makolo kuti amubwenzere ndalama ndi nkhuku za banja zisapitilirenso zomwe zinachititsa makolo ake kukatokoza nkhaniyi kwa apolisi.

A Magistrate Godfrey Nyirenda anagamula kuti pansi pa kusintha kwa Penal Code ka 2023, kukhulupirira kuti mtsikana siwamkulu potengera chilungamo choti anabadwa 2008 osati 2006 ndipo pali mulandu okuti ayankhe posatengera chiphatso chauzika popeza mwanayo ananama zaka chabe Cholinga athe kuvota Chaka chatha.

Chimpeni akusungidwa m’ndende akuyembekezera chilango Lolemba likudzali.

Pankhaniyi lawyer Ayuba wazipeleka kukayimira bambo omangidwayu pa court mwa ulere.

The NPA says they want Shebeshxt to get a long jail sentence 😳💔They believe their case is very strong.Shebe was arrested...
14/11/2025

The NPA says they want Shebeshxt to get a long jail sentence 😳💔
They believe their case is very strong.

Shebe was arrested after a road-rage shooting where a man was shot in the stomach and is still in ICU 😢.
The NPA says they have more charges they might add, and they are ready to fight this case in court.

Right now Shebe is still behind bars, and the state says he has many old cases that will also be used against him.

This time it looks very serious… things are not looking good for him 😔⚠️

Worst time for lekompo😓 Kharishma at Hospital,Shebe in Jail and Dr Nel in the Grave🥺💔💔
14/11/2025

Worst time for lekompo😓 Kharishma at Hospital,Shebe in Jail and Dr Nel in the Grave🥺💔💔

“Mzika iliyonse ya America ilandila $2,000 kuchokera ku misonkho ya katundu wochokera kunja”President Donald Trump wati ...
14/11/2025

“Mzika iliyonse ya America ilandila $2,000 kuchokera ku misonkho ya katundu wochokera kunja”

President Donald Trump wati mzika iliyonse ya America idzalandira $2,000 (pafupifupi K8 million) ngati dividend kuchokera ku tariff revenue — ndalama zimene boma limapeza kuchokera ku misonkho yomwe imayikidwa pa katundu wochoka kapena kulowa m’dziko kuchokera kunja.

Iye wati Mzika nazo zipakule gawo lawo

Nkulu mukumuona apayu  dzina lake  ndi Hazwell ndipo kutengera ndi zomwe wanena James C Makopa akuti ameneyo ndie mwini ...
13/11/2025

Nkulu mukumuona apayu dzina lake ndi Hazwell ndipo kutengera ndi zomwe wanena James C Makopa akuti ameneyo ndie mwini Bakili Muluzi TV.

Abambo awiri omwe ndi a pachibale Siyabonga komanso Malusi  Ndimande awatsegulira mlandu wakupha woyimba wodziwika bwino...
13/11/2025

Abambo awiri omwe ndi a pachibale Siyabonga komanso Malusi Ndimande awatsegulira mlandu wakupha woyimba wodziwika bwino wa mdziko la South Africa AKA (Kiernan Forbes).

Awiriwa omwe akwidzingidwa mdziko la Eswatini komwe amabisala akuwaganizira kuti mchaka cha 2023 adapha AKA komanso mzake mu mzinda wotchedwa Durban ku South Africa.

Apolisi mdzikolo ati mukufufuza kwao anapeza kuti anthuwa ankafuna kupha AKA yekha koma mwatsoka adaphanso mzake wa woyimbayu.

Abambo awiriwa abweleranso ku bwalo la milandu pa 25 November mwezi uno kuti akamve ngati nkoyenera kupatsidwa belo pa mlanduwu.

AKA yemwe anaimbaponso mdziko muno adaomberedwa pamodzi ndi mzakeyu panja pa malo ena wodyera.

'HRDC imagwira ntchito mosata malamuro oyendesera dziko lino kotero sitimadana ndi a Muntharika':-Michael Kayiyatsa nkul...
13/11/2025

'HRDC imagwira ntchito mosata malamuro oyendesera dziko lino kotero sitimadana ndi a Muntharika':-

Michael Kayiyatsa nkulu wa bungwe lomenyera ufulu la HRDC walankhulapo pankhani yomwe ikuzungulira kuti iwo amadana ndi chipani cha DPP komanso a Mutharika.

Mau awo a Kayiyatsa ati ":-

"bungwe lathu limagwira ntchito mosata malamuro oyendesera dziko lino ndipo Amalawi maziwa bwino lomwe kuti HRDC yomwe inali nthawi ya MCP ndiyomwe iliso pano.

HRDC yakhala likudzuzula boma pa a Chakwera choncho tichita chimodzimodzi Kwa a Mutharika ngati Pali kufunika kutero ndicholinga choyimira m'malawi osauka.

'HRDC sichipani Cha ndale kotero Amalawi asiye kulowetsa ndale pa ntchito za mabungwe omwe siaboma.':- anatsendera motero a Kaiyatsa.

13/11/2025

Ma ripoti amati Mzinda oopsa kwambiri padziko lapansi ndi Tijuana.
Koma kodi amau mau mumadziwa kuti Salima ya ku jozi(kepi tawuni) nde mzinda oopsa???
Salima ya kumeneko pa tsiku lililonse kumaomberedwa komanso phedwa anthu oposera 20

Ifo iyi amaliongo akumeneko samafuna olo pang'ono kuti izioneka,chifukwaa ndi mzinda umene uli mu topu yoyambirila mu afilika kumene amalandila alendo ochuluka, mmalo mwake mzinda oopsa anauika kukhala johanizibeki ndi ena

Address

Midrand

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Faluku posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share